Yobu 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ngati ndayesa golide chinthu chodalira,Kapena ngati ndanena kwa golide kuti, ‘Ndimadalira iwe,’+ Salimo 52:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+ Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+