Miyambo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+ Yesaya 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Woyera wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu mwakana mawu anga+ n’kumadalira kuba mwachinyengo. Mukudalira zinthu zachinyengo ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezo.+
31 Wobera munthu wosauka mwachinyengo amanyoza amene anamupanga,+ koma wokomera mtima munthu wosauka amalemekeza amene anamupanga.+
12 Chotero Woyera wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu mwakana mawu anga+ n’kumadalira kuba mwachinyengo. Mukudalira zinthu zachinyengo ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezo.+