4 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Yuda+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anakana lamulo la Yehova+ ndiponso sanasunge malangizo ake koma anasocheretsedwa ndi mabodza+ amene makolo awo anali kutsatira.+