2 Mbiri 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musakhale ngati makolo anu+ ndi abale anu amene anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wa makolo awo, mwakuti anawachititsa kukhala chinthu chodabwitsa+ monga mmene mukuoneramu. Yeremiya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 koma iwo anapitirizabe kuumitsa mitima yawo+ ndi kutsatira mafano a Baala,+ zinthu zimene anaphunzitsidwa ndi makolo awo.+
7 Musakhale ngati makolo anu+ ndi abale anu amene anachita zosakhulupirika kwa Yehova Mulungu wa makolo awo, mwakuti anawachititsa kukhala chinthu chodabwitsa+ monga mmene mukuoneramu.
14 koma iwo anapitirizabe kuumitsa mitima yawo+ ndi kutsatira mafano a Baala,+ zinthu zimene anaphunzitsidwa ndi makolo awo.+