Oweruza 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ana a Isiraeli anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anayamba kutumikira Abaala+ ndi mizati yopatulika.+ 1 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’ Hoseya 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+
7 Chotero ana a Isiraeli anachita zoipa pamaso pa Yehova, ndipo anaiwala Yehova Mulungu wawo,+ moti anayamba kutumikira Abaala+ ndi mizati yopatulika.+
10 Choncho anayamba kufuulira Yehova kuti awathandize,+ ndipo anati, ‘Tachimwa,+ pakuti tasiya Yehova kuti titumikire Abaala+ ndi zifaniziro za Asitoreti.+ Tsopano tilanditseni+ m’manja mwa adani athu, kuti tikutumikireni.’
2 “Pamene iye anali kuitanidwa kwambiri,+ m’pamenenso anapitiriza kuchoka.+ Anayamba kupereka nsembe kwa zifaniziro za Baala+ ndipo anayamba kufukiza nsembe zautsi kwa zifaniziro zogoba.+