Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 12:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Yerobowamu anapereka nsembe pa tsiku la 15, m’mwezi wa 8 womwe anausankha yekha.+ Anapereka nsembezo paguwa limene anamanga ku Beteli. Ndipo anakonzera chikondwerero ana a Isiraeli ndi kupereka nsembe zautsi kuti afukize paguwalo.+

  • Yesaya 65:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 chifukwa cha zolakwa zawo ndi zolakwa za makolo awo pa nthawi imodzi,”+ watero Yehova. “Popeza afukiza nsembe zautsi pamapiri ndipo andinyoza+ pazitunda,+ ine ndidzawayezera mphoto yawo choyamba, n’kuiika pachifuwa pawo.”+

  • Yeremiya 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika.

  • Hoseya 13:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano anthu ake akuchita machimo ena ndipo akugwiritsa ntchito siliva wawo popanga zifanizo zachitsulo chosungunula.+ Zifanizo zimenezo ndi mafano opangidwa mogwirizana ndi maganizo awo,+ koma zonsezi ndi ntchito za amisiri.+ Iwo amauza mafanowo kuti, ‘Amuna opereka nsembe apsompsone mafano a ana ang’ombe.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena