Deuteronomo 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+ Yesaya 41:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Onsewo ali ngati chinthu choti kulibeko. Ntchito zawo si kanthu. Mafano awo opangidwa ndi zitsulo zosungunula ali ngati mphepo ndiponso zinthu zomwe si zenizeni.+ Yeremiya 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iwo ndi achabechabe, ntchito yoyenera kutonzedwa.+ Mulungu akadzatembenukira kwa iwo, adzawawononga.+
21 Iwo andichititsa nsanje ndi milungu yachabe.+Andisautsa ndi mafano awo opanda pake.+Ndipo ine ndidzawachititsa nsanje ndi anthu achabe,+Ndidzawakhumudwitsa ndi mtundu wopusa.+
29 Onsewo ali ngati chinthu choti kulibeko. Ntchito zawo si kanthu. Mafano awo opangidwa ndi zitsulo zosungunula ali ngati mphepo ndiponso zinthu zomwe si zenizeni.+
15 Iwo ndi achabechabe, ntchito yoyenera kutonzedwa.+ Mulungu akadzatembenukira kwa iwo, adzawawononga.+