Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+

  • Hoseya 2:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+

  • Aroma 9:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zilinso monga mmene ananenera m’buku la Hoseya kuti: “Anthu amene si anthu anga+ ndidzawatcha ‘anthu anga,’ ndipo mkazi amene sanali wokondedwa ndidzamutcha ‘wokondedwa.’+

  • Aroma 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno ndifunse, Kodi anapunthwa mpaka kugweratu?+ Ayi! Koma chifukwa cha kulakwa kwawo+ pali chipulumutso kwa anthu a mitundu ina,+ kuti olakwawo achite nsanje.+

  • 1 Petulo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena