Hoseya 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+ Mateyu 21:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ichi n’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu n’kuperekedwa kwa mtundu wobala zipatso zake.+ 1 Petulo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+
23 Pamenepo ndidzamufesa ngati mbewu zanga padziko lapansi.+ Ndidzachitira chifundo amene sanasonyezedwe chifundo+ ndipo ndidzauza anthu amene si anthu anga kuti: “Inu ndinu anthu anga,”+ ndipo iwo adzayankha kuti: “Inu ndinu Mulungu wathu.”’”+
43 Ichi n’chifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu n’kuperekedwa kwa mtundu wobala zipatso zake.+
10 Pakuti kale simunali mtundu, koma tsopano ndinu mtundu wa anthu a Mulungu.+ Munali anthu amene sanakuchitireni chifundo, koma tsopano ndinu amene mwachitiridwa chifundo.+