Aroma 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Komabe ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje kudzera mwa anthu omwe si mtundu. Ndidzaputa mkwiyo wanu woopsa kudzera mwa mtundu wopusa.”+
19 Komabe ndifunse kuti, Kodi si zoona kuti Aisiraeli anadziwa?+ Choyamba Mose anati: “Ndidzakuchititsani nsanje kudzera mwa anthu omwe si mtundu. Ndidzaputa mkwiyo wanu woopsa kudzera mwa mtundu wopusa.”+