Salimo 119:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Odala ndi anthu osalakwitsa kanthu m’njira zawo,+Anthu amene akutsatira chilamulo cha Yehova.+