Salimo 119:97 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!+Ndimasinkhasinkha chilamulocho tsiku lonse.+ Salimo 128:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 128 Wodala ndi aliyense woopa Yehova,+Amene amayenda m’njira za Mulungu.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga+ ndimasangalala kwambiri+ ndi chilamulo cha Mulungu, Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+
25 Koma woyang’anitsitsa m’lamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu, amene amalimbikira kutero, adzakhala wosangalala+ polichita chifukwa chakuti sali wongomva n’kuiwala, koma wochita.+