Genesis 39:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’nyumba muno mulibe woyang’anira woposa ine, ndipo mbuye wanga anaika chilichonse m’manja mwanga kupatulapo inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake.+ Ndiye ndingachitirenji choipa chachikulu chonchi n’kuchimwira Mulungu?”+ Agalatiya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, amene akugwiritsitsa chikhulupiriro akudalitsidwa+ limodzi ndi Abulahamu wokhulupirikayo.+ Aheberi 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+
9 M’nyumba muno mulibe woyang’anira woposa ine, ndipo mbuye wanga anaika chilichonse m’manja mwanga kupatulapo inuyo, chifukwa ndinu mkazi wake.+ Ndiye ndingachitirenji choipa chachikulu chonchi n’kuchimwira Mulungu?”+
9 Chotero, amene akugwiritsitsa chikhulupiriro akudalitsidwa+ limodzi ndi Abulahamu wokhulupirikayo.+
5 Ndipo Mose monga wantchito+ anali wokhulupirika m’nyumba yonse ya Mulungu. Utumiki wakewo unali umboni wa zinthu zimene zidzalankhulidwe m’tsogolo.+