Miyambo 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+ Maliko 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi,’+ moti salinso awiri, koma thupi limodzi.
29 N’chimodzimodzi ndi aliyense wogona ndi mkazi wa mnzake.+ Aliyense wokhudza mkaziyo adzalangidwa.+