2 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano lupanga+ silidzachoka panyumba yako mpaka kalekale.+ Chimenechi n’chotsatira cha zimene unachita chifukwa chondinyoza mwa kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala mkazi wako.’ Miyambo 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye sadzavomera dipo* lamtundu uliwonse, ndipo sadzalola ngakhale utapereka mphatso yaikulu bwanji. Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
10 Tsopano lupanga+ silidzachoka panyumba yako mpaka kalekale.+ Chimenechi n’chotsatira cha zimene unachita chifukwa chondinyoza mwa kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala mkazi wako.’
35 Iye sadzavomera dipo* lamtundu uliwonse, ndipo sadzalola ngakhale utapereka mphatso yaikulu bwanji.
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+