Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 13:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Koma Yehonadabu+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide anati: “Inu mbuyanga musaganize kuti ndi ana onse a mfumu amene aphedwa, pakuti ndi Aminoni yekha amene wafa.+ Abisalomu ndi amene walamula zimenezi kuti zichitike pakuti anakonzeratu+ zimenezi kuyambira pa tsiku limene Aminoniyo anachititsa manyazi+ Tamara mlongo wake.+

  • 2 Samueli 18:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Pamenepo mfumu inasokonezeka ndipo inakwera m’chipinda cha padenga+ cha pachipata ndi kuyamba kulira. Mfumu inali kuyenda n’kumanena kuti: “Mwana wanga Abisalomu, mwana wanga, mwana wanga+ Abisalomu! Haa! Zikanakhala bwino ndikanafa ndine m’malo mwa iwe, Abisalomu mwana wanga, mwana wanga!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena