Yohane 12:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+
26 Ngati munthu wafuna kunditumikira ine, anditsatire, ndipo kumene ine ndidzakhala, mtumiki wanga adzakhalanso komweko.+ Aliyense wonditumikira ine, Atate adzamulemekeza.+