Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zinthu zinapitiriza kumuyendera bwino Yehosafati ndipo mphamvu zake zinapitiriza kukula kwambiri.+ Iye anayamba kumanga m’dziko la Yuda malo okhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndiponso mizinda yosungirako zinthu.+

  • 2 Mbiri 26:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kuwonjezera apo Uziya anamanga nsanja+ ku Yerusalemu pafupi ndi Chipata cha Pakona,+ Chipata cha Kuchigwa,+ ndiponso pafupi ndi Mchirikizo wa Khoma, ndipo nsanjazo anazilimbitsa.

  • Nehemiya 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso andipatse kalata yopita kwa Asafu amene akuyang’anira nkhalango ya mfumu, kuti akandipatse mitengo yokamangira zipata za Nyumba ya Chitetezo Champhamvu+ ya kukachisi,+ mpanda+ wa mzindawo ndiponso nyumba imene ndizikakhalamo.” Choncho mfumu inandipatsa makalatawo, chifukwa Mulungu anandikomera mtima.+

  • Machitidwe 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mkanganowo utakula kwambiri, mkulu wa asilikali anachita mantha kuti anthuwo amukhadzulakhadzula Paulo. Chotero analamula asilikali+ kuti apite komweko kuti akamuchotse pakati pawo ndi kumubweretsa kumpanda wa asilikali.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena