2 Mbiri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri m’dziko la Yuda,+ chifukwa m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse, komanso palibe anachita naye nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anam’patsa mpumulo.+
6 Kenako anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri m’dziko la Yuda,+ chifukwa m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse, komanso palibe anachita naye nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anam’patsa mpumulo.+