Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Tsopano Yoswa anali atakalamba ndiponso anali ndi zaka zambiri.+ Apa n’kuti patapita masiku ambiri kuchokera pamene Yehova anapatsa Aisiraeli mpumulo+ pakati pa adani awo onse owazungulira.

  • 2 Mbiri 15:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ayuda onse anayamba kusangalala+ chifukwa cha zimene analumbirazo popeza analumbira ndi mtima wawo wonse, komanso chifukwa chakuti anafunafuna Mulungu mokondwa kwambiri moti iye analola kuti amupeze.+ Choncho Yehova anapitiriza kuwapatsa mpumulo pakati pa adani awo onse owazungulira.+

  • Salimo 46:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Akuletsa nkhondo mpaka kumalekezero a dziko lapansi.+

      Wathyola uta ndi kuduladula mkondo.+

      Ndipo watentha magaleta pamoto.+

  • Miyambo 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehova akasangalala ndi njira za munthu,+ amachititsa ngakhale adani a munthuyo kukhala naye pa mtendere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena