Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Samala kuti usalankhule mawu achabe mumtima mwako+ kuti, ‘Chaka cha 7, chaka choti anthu angongole amasuke chayandikira,’+ kuti usaolowere manja m’bale wako wosaukayo,+ osam’patsa kalikonse. Pamenepo iye adzafuulira Yehova chifukwa cha zimene iweyo wam’chitira+ ndipo udzapezeka kuti wachimwa.+

  • Mateyu 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma ngati diso lako lili loipa,+ thupi lako lonse lidzachita mdima. Choncho ngati kuwala kumene kuli mwa iwe ndiko mdima, ndiye kuti mdimawo ndi wandiweyani!+

  • Mateyu 20:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 kuti, ‘Omalizirawa agwira ntchito ola limodzi lokha, koma mwawapatsa malipiro ofanana ndi ife amene tagwira ntchito yakalavulagaga tsiku lonse padzuwa lotentha!’

  • Maliko 7:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.

  • 2 Petulo 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena