Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+ Mateyu 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi n’kosaloleka kuchita zimene ndikufuna ndi zinthu zanga? Kapena diso lako lachita njiru+ chifukwa chakuti ndine wabwino?’+ Maliko 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena. 2 Petulo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
15 Kodi n’kosaloleka kuchita zimene ndikufuna ndi zinthu zanga? Kapena diso lako lachita njiru+ chifukwa chakuti ndine wabwino?’+
22 zachigololo, kusirira kwa nsanje,+ kuchita zoipa, chinyengo, khalidwe lotayirira,+ diso la kaduka, mnyozo, kudzikweza, ndiponso kuchita zinthu mosaganizira ena.
14 Ali ndi maso odzaza ndi chigololo+ komanso olephera kupewa kuchita tchimo,+ ndipo amakopa anthu apendapenda. Ali ndi mtima wophunzitsidwa kusirira mwansanje.+ Iwo ndi ana otembereredwa.+