Miyambo 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+ Yeremiya 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ine Yehova ndimafufuza mtima+ ndi kusanthula impso.+ Munthu aliyense ndimamuchitira zinthu monga mwa zochita zake,+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+ Mateyu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+
23 Uteteze mtima wako kuposa zonse zimene ziyenera kutetezedwa,+ pakuti mumtimamo ndiye muli akasupe a moyo.+
10 Ine Yehova ndimafufuza mtima+ ndi kusanthula impso.+ Munthu aliyense ndimamuchitira zinthu monga mwa zochita zake,+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zake.+
19 Mwachitsanzo, maganizo oipa, za kupha anthu, za chigololo, za dama, za kuba, maumboni onama, ndi zonyoza Mulungu,+ zimachokera mumtima.+