Salimo 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+ Yeremiya 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+
12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+
19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+