Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 16:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Yehova anauza Samueli kuti: “Usaone maonekedwe ake ndi kutalika kwa msinkhu wake,+ pakuti ine ndamukana ameneyu. Chifukwa mmene munthu amaonera si mmene Mulungu amaonera.+ Munthu amaona zooneka ndi maso,+ koma Yehova amaona mmene mtima ulili.”+

  • 1 Mbiri 28:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Ndipo iwe Solomo mwana wanga, dziwa+ Mulungu wa bambo wako, um’tumikire+ ndi mtima wathunthu+ ndi moyo wosangalala,+ chifukwa Yehova amasanthula mitima yonse+ ndipo amazindikira maganizo a munthu ndi zolinga zake zonse.+ Ukam’funafuna, adzalola kuti um’peze,+ koma ukam’siya+ adzakutaya kosatha.+

  • Salimo 139:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndifufuzeni, inu Mulungu, ndi kudziwa mtima wanga.+

      Ndisanthuleni ndi kudziwa malingaliro anga amene akundisowetsa mtendere,+

  • Miyambo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+

  • Miyambo 21:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Njira iliyonse ya munthu imaoneka yowongoka m’maganizo mwake,+ koma Yehova amafufuza mitima.+

  • Aroma 8:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma iye amene amasanthula mitima+ amadziwa zimene mzimu ukutanthauza,+ chifukwa umachonderera m’malo mwa oyera mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena