2 Akorinto 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+ 2 Akorinto 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukuona zinthu mogwirizana ndi maonekedwe ake akunja.+ Ngati aliyense amakhulupirira mumtima mwake kuti ndi wotsatira Khristu, adziwenso kuti, monga mmene iye alili wotsatira Khristu, ifenso ndife otsatira Khristu.+
12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+
7 Mukuona zinthu mogwirizana ndi maonekedwe ake akunja.+ Ngati aliyense amakhulupirira mumtima mwake kuti ndi wotsatira Khristu, adziwenso kuti, monga mmene iye alili wotsatira Khristu, ifenso ndife otsatira Khristu.+