Salimo 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso sangalala mwa Yehova,+Ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.+ Salimo 73:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+
25 Winanso ndani kumwambako amene ali kumbali yanga?+Palibe wina wondisangalatsa padziko lapansi koma inu nokha.+