Salimo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti amadzinyenga yekha,+Ndipo sazindikira cholakwa chake ndi kudana nacho.+ Miyambo 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Njira zonse za munthu zimaoneka zoyera m’maganizo mwake,+ koma Yehova amafufuza zolinga zake.+ Miyambo 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pali m’badwo umene umadziona kuti ndi woyera,+ koma sunasambe kuti uchotse ndowe zake.+