Salimo 36:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti amadzinyenga yekha,+Ndipo sazindikira cholakwa chake ndi kudana nacho.+ Yesaya 65:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo amanena kuti, ‘Khala pawekha. Usandiyandikire, kuti ndingakupatsire chiyero changa.’+ Iwo ali ngati utsi m’mphuno mwanga,+ ngati moto woyaka tsiku lonse.+ Luka 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo iye anawauza kuti: “Inu mumadzitcha olungama pamaso pa anthu,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene chili chapamwamba kwa anthu n’chonyansa m’maso mwa Mulungu.+ 2 Timoteyo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 achiwembu,+ osamva za ena, odzitukumula ndiponso onyada,+ okonda zosangalatsa, m’malo mokonda Mulungu,+ 1 Yohane 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikanena kuti: “Tilibe uchimo,”+ ndiye kuti tikudzinamiza+ ndipo mwa ife mulibe choonadi.
5 Iwo amanena kuti, ‘Khala pawekha. Usandiyandikire, kuti ndingakupatsire chiyero changa.’+ Iwo ali ngati utsi m’mphuno mwanga,+ ngati moto woyaka tsiku lonse.+
15 Pamenepo iye anawauza kuti: “Inu mumadzitcha olungama pamaso pa anthu,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene chili chapamwamba kwa anthu n’chonyansa m’maso mwa Mulungu.+
4 achiwembu,+ osamva za ena, odzitukumula ndiponso onyada,+ okonda zosangalatsa, m’malo mokonda Mulungu,+