1 Mafumu 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Palibe munthu wolungama padziko lapansi amene amachita zabwino zokhazokha osachimwa.+
46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+