Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 6:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa mdani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko lakutali kapena lapafupi,+

  • Salimo 51:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+

      Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+

  • Salimo 130:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Inu Ya, mukanakhala kuti mumayang’anitsitsa zolakwa,+

      Ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+

  • Salimo 143:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Musandiimbe mlandu ine mtumiki wanu,+

      Pakuti palibe aliyense wamoyo amene angakhale wolungama pamaso panu.+

  • Miyambo 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndani anganene kuti: “Ndayeretsa mtima wanga,+ ndadziyeretsa ku tchimo langa”?+

  • Aroma 3:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti onse ndi ochimwa+ ndipo ndi operewera pa ulemerero wa Mulungu.+

  • Yakobo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.

  • 1 Yohane 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tikanena kuti: “Tilibe uchimo,”+ ndiye kuti tikudzinamiza+ ndipo mwa ife mulibe choonadi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena