Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Palibe munthu wolungama padziko lapansi amene amachita zabwino zokhazokha osachimwa.+ Aroma 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye zikatero? Kodi tili pabwino kuposa ena?+ Ayi! Pakuti tanena kale poyamba paja kuti onse, Ayuda ndi Agiriki, ndi ochimwa+
9 Ndiye zikatero? Kodi tili pabwino kuposa ena?+ Ayi! Pakuti tanena kale poyamba paja kuti onse, Ayuda ndi Agiriki, ndi ochimwa+