Genesis 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Mulungu anaona kuti zonse zimene anapanga zinali zabwino kwambiri.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku la 6. Yesaya 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+
31 Ndiyeno Mulungu anaona kuti zonse zimene anapanga zinali zabwino kwambiri.+ Panali madzulo ndiponso panali m’mawa, tsiku la 6.
6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+