Salimo 90:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Msipuwo umaphuka ndi kutsitsimuka m’mawa.+Madzulo umafota kenako umauma.+ Yakobo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+
10 ndipo wachuma+ akondwere chifukwa tsopano watsitsidwa, chifukwa mofanana ndi duwa la zomera, wachumayo adzafota.+