Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+ Yesaya 57:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ukamafuula popempha thandizo, zinthu zimene unasonkhanitsa sizidzakupulumutsa,+ koma mphepo idzaziulutsa zonsezo+ ndipo mpweya udzazitenga. Koma munthu wobisala mwa ine+ adzalandira dziko ndipo adzatenga phiri langa loyera.+
13 Ukamafuula popempha thandizo, zinthu zimene unasonkhanitsa sizidzakupulumutsa,+ koma mphepo idzaziulutsa zonsezo+ ndipo mpweya udzazitenga. Koma munthu wobisala mwa ine+ adzalandira dziko ndipo adzatenga phiri langa loyera.+