Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ochita zoipa adzaphedwa.+Koma oyembekezera Yehova ndi amene adzalandire dziko lapansi.+ Yesaya 58:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+
9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+