Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+

      Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+

  • Salimo 37:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+

      Ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.+

  • Yesaya 57:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ukamafuula popempha thandizo, zinthu zimene unasonkhanitsa sizidzakupulumutsa,+ koma mphepo idzaziulutsa zonsezo+ ndipo mpweya udzazitenga. Koma munthu wobisala mwa ine+ adzalandira dziko ndipo adzatenga phiri langa loyera.+

  • Yesaya 58:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 pamenepo mudzasangalala kwambiri mwa Yehova.+ Ine ndidzakuchititsani kuti mukwere m’malo okwezeka a dziko lapansi,+ ndipo ndidzakuchititsani kuti mudye zochokera m’cholowa cha Yakobo kholo lanu,+ pakuti pakamwa pa Yehova panena zimenezi.”+

  • Mateyu 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Odala ndi anthu amene ali ofatsa,+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena