Yobu 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi iwo amakhala ngati udzu wouluzika ndi mphepo?+Kapena ngati mankhusu* ouluka ndi mphepo yamkuntho? Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+
18 Kodi iwo amakhala ngati udzu wouluzika ndi mphepo?+Kapena ngati mankhusu* ouluka ndi mphepo yamkuntho?