Yesaya 58:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+
6 “Kusala kudya kumene ine ndimafuna n’kotere: Mumasule maunyolo ozunzira anzanu,+ mumasule zingwe za goli,+ mumasule anthu opsinjika kuti azipita kwawo,+ ndipo goli lililonse mulithyole pakati.+