Yeremiya 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova anauza Yeremiya mawu pamene Mfumu Zedekiya inachita pangano ndi anthu onse a mu Yerusalemu kuti alengeze ufulu,+ Ezekieli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+
8 Yehova anauza Yeremiya mawu pamene Mfumu Zedekiya inachita pangano ndi anthu onse a mu Yerusalemu kuti alengeze ufulu,+
8 ngati salandira chiwongoladzanja akabwereketsa zinthu,+ ndiponso sakongoza zinthu mwa katapira,*+ ngati sachita zopanda chilungamo,+ ngati amachita chilungamo chenicheni poweruza munthu ndi mnzake,+