1 Mafumu 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+ Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Palibe munthu wolungama padziko lapansi amene amachita zabwino zokhazokha osachimwa.+ Yakobo 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.
46 “Anthu anu akakuchimwirani+ (popeza palibe munthu amene sachimwa)+ inu n’kuwakwiyira, n’kuwapereka kwa adani, adani awowo n’kuwagwira kupita nawo kudziko la adani, lakutali kapena lapafupi,+
5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.