Miyambo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani anganene kuti: “Ndayeretsa mtima wanga,+ ndadziyeretsa ku tchimo langa”?+