Yobu 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndani anabadwa ali woyera kuchokera mwa munthu wodetsedwa?+Palibe ndi mmodzi yemwe. Aroma 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Palibe munthu wolungama ndi mmodzi yemwe.+