Genesis 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Adamu atakhala ndi moyo zaka 130, anabereka mwana wamwamuna m’chifaniziro chake, wofanana naye. Anamutcha dzina lake Seti.+ Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Yohane 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chobadwa mwa thupi n’chanyama, ndipo chobadwa mwa mzimu n’chauzimu.+ Aroma 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .
3 Adamu atakhala ndi moyo zaka 130, anabereka mwana wamwamuna m’chifaniziro chake, wofanana naye. Anamutcha dzina lake Seti.+
5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
12 Ndiye chifukwa chake monga mmene uchimo unalowera m’dziko kudzera mwa munthu mmodzi,+ ndi imfa+ kudzera mwa uchimo, imfayo n’kufalikira kwa anthu onse chifukwa onse anachimwa+ . . .