-
Ezara 8:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ndinatero pakuti ndinachita manyazi kupempha kwa mfumu gulu lankhondo+ ndi okwera pamahatchi+ kuti atithandize kumenyana ndi adani m’njira, chifukwa tinali titauza mfumuyo kuti: “Dzanja+ la Mulungu wathu lili ndi onse om’funafuna kuti awachitire zabwino,+ koma mkwiyo wake+ wamphamvu umayakira onse omusiya.”+
-