Malaki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?” Yakobo 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+
7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”
8 Yandikirani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikirani.+ Yeretsani manja anu ochimwa inu,+ ndipo yeretsani mitima yanu,+ okayikakayika inu.+