Malaki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuyambira mʼmasiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawatsatire.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Koma inu mukunena kuti: “Tingabwerere bwanji?” Malaki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:7 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, ptsa. 20-214/15/1995, tsa. 1812/1/1992, ptsa. 11-128/1/1992, ptsa. 28-30
7 Kuyambira mʼmasiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawatsatire.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndidzabwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. Koma inu mukunena kuti: “Tingabwerere bwanji?”
3:7 Nsanja ya Olonda,5/1/2002, ptsa. 20-214/15/1995, tsa. 1812/1/1992, ptsa. 11-128/1/1992, ptsa. 28-30