Mateyu 25:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pamenepo iye adzawayankha kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Popeza simunachitire zimenezo mmodzi wa aang’ono awa,+ simunachitirenso+ ine.’+ Yakobo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+
45 Pamenepo iye adzawayankha kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Popeza simunachitire zimenezo mmodzi wa aang’ono awa,+ simunachitirenso+ ine.’+