Deuteronomo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa chake n’chakuti, sanakuthandizeni+ ndi mkate ndi madzi pamene munali pa ulendo mutatuluka mu Iguputo,+ ndiponso chifukwa chakuti analemba ganyu Balamu mwana wa Beori, amene kwawo ndi ku Petori ku Mesopotamiya kuti akutemberereni.+ 2 Akorinto 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.” Aheberi 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+
4 Chifukwa chake n’chakuti, sanakuthandizeni+ ndi mkate ndi madzi pamene munali pa ulendo mutatuluka mu Iguputo,+ ndiponso chifukwa chakuti analemba ganyu Balamu mwana wa Beori, amene kwawo ndi ku Petori ku Mesopotamiya kuti akutemberereni.+
20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.”
11 Pakuti onse, woyeretsayo ndi amene akuyeretsedwawo,+ amachokera kwa mmodzi.+ Pa chifukwa chimenechi, iye sachita manyazi kuwatcha “abale,”+