14 Koma tiyamike Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera+ pamodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadirira kupambana.+ Kudziwa Mulungu kuli ngati fungo lonunkhira bwino ndipo kudzera mu ntchito yathu fungoli likufalikira paliponse.+